Mawu Amunsi
a Mu 2013, anchito odzipeleka oposa 230,000 a ku United States analoledwa kugwila nchito yomanga limodzi ndi Makomiti a Nchito Yomanga Nyumba za Ufumu okwana 132 a m’dzikolo. M’dzikolo, makomiti amenewo amayang’anila nchito yomanga Nyumba za Ufumu pafupifupi 75 ndi kukonza zina pafupifupi 900 caka ciliconse.