Mawu Amunsi
a Madokotala ena angaone mbali zinayi zikulu-zikulu za magazi kukhala tumbali tung’ono-tung’ono. Conco, mungafunike kufotokoza cosankha canu cokana kuikidwa magazi athunthu, kapena mbali zake zinayi zikulu-zikulu, zochedwa maselo ofiila, maselo oyela, maselo ochedwa platelets, komanso madzi ochedwa plasma.