Mawu Amunsi a Kuti mumve zambili pa tanthauzo la dzina la Mulungu limeneli, na cifukwa cimene analicotsela m’ma Baibo ena, onani Mutu 1 wa Buku Lothandiza Pophunzila Mau a Mulungu.