Mawu Amunsi
a Kuti mudziŵe zambili za mmene Ufumu udzapangitsile cifunilo ca Mulungu kucitika padziko lapansi, onani nkhani 8 m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Mukhoza kupeza buku limeneli kapena kulitenga pa webu saiti yathu ya www.pr2711.com.