Mawu Amunsi
c M’nthawi ya Yesu, talente imodzi inali kulemela madinari pafupifupi 6,000. Ngati wanchito wamba anali kulandila dinari imodzi patsiku, ndiye kuti akanafunika kugwila nchito zaka 20 kuti alandile talente imodzi.