Mawu Amunsi
a Filipi linali dela lolamulidwa ndi ufumu wa Roma. Zioneka kuti Akristu ena mumpingo wa kumeneko anapatsidwa mwai wokhala nzika za Roma. Cifukwa cakuti anakhala nzika anali ndi mwai wocita zinthu zina zimene abale ena sanaloledwe kucita.