Mawu Amunsi
c Nkhondo imene inatsatilapo ikuchulidwa kaŵili m’Baibulo, ikufotokozedwa m’caputala 4 ndi m’nyimbo ya Debora ndi Baraki m’caputala 5 ca buku la Oweluza. Macaputala aŵiliwa ndi ogwilizana kwambili, koma caputala ciliconse cikufotokoza zinthu zimene sizinachulidwe m’caputala cina.