Mawu Amunsi
a Inali nthawi ya m’madzulo. Baibulo silionetsa utali wa nthawi imene Rabeka anakhala ku citsime. Silionetsanso kuti anthu a m’banja lake anali atagona pamene iye anamaliza nchitoyo, kapena kuti wina wa m’banja lake anamulondola cifukwa cocedwa kufika panyumba.