Mawu Amunsi
b Eliezere sanachulidwe dzina lake m’nkhani yonseyi, koma aoneka kuti ndiye mtumiki amene anatumidwa. Abulahamu anauza Eliezere kuti ndiye adzatenge coloŵa iye akadzafa. Conco, iye anali mtumiki wamkulu koposa komanso wodalilika wa Abulahamu. Umu ndi mmene mtumikiyu akufotokozedwela m’nkhani ino.—Genesis 15:2; 24: 2-4.