Mawu Amunsi
a Buku lochedwa Fivefold Psalter linali ndi madanga 5 pa tsamba lililonse. M’madangawo munali mau a m’buku la Masalimo ocokela m’mabaibo asanu a Cilatini. M’bukuli munalinso chati ya maina audindo a Mulungu, kuphatikizapo zilembo zinayi za Ciheberi zoimila dzina la Mulungu.