Mawu Amunsi
b Patapita zaka 5, mu 1535, womasulila wina wa ku France, dzina lake Olivétan, anatulutsa Baibo imene anaimasulila kucokela ku zinenelo zoyambilila. Iye anali kudalila kwambili Baibo ya Lefèvre pomasulila Malemba Acigiriki.