Mawu Amunsi
a Kuti mudziŵe zambili pankhani ya zizindikilo za masiku otsiliza, ŵelengani nkhani 9 yakuti; “Kodi Tili mu ‘Masiku Otsiliza’?” m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, lofalitsidwa na Mboni za Yehova, ndipo lilipo pa webusaiti yathu ya www.jw.org.