Mawu Amunsi
a Anthu ena amapeleka mphatso pa masiku a kubadwa ndi pa zikondwelelo za pa maholide. Komabe, kambili zikondwelelo zimenezi zimaloŵetsamo zocitika zotsutsana na zimene Baibo imaphunzitsa. Onani nkhani yakuti “Mafunso Ocokela Kwa Aŵelengi—Kodi Akhristu Ayenela Kukondwelela Khrisimasi?” m’magazini ino.