Mawu Amunsi
a Pa kuvina kodukulilana pa mendo kumeneku kochedwa lap dancing, “nthawi zambili mkazi wovala twamkati cabe amakhala pa mendo pa mwamuna n’kumavina modukula.” Malinga na mmene zingacitikile, kuvina kwa lap dancing kungafanane ndi khalidwe la ciwelewele, ndipo kungafunikile komiti ya ciweluzo. Conco, Mkhristu aliyense amene watengako mbali pa mcitidwe umenewu afunika kukapempha thandizo kwa akulu.—Yak. 5:14, 15.