Mawu Amunsi
b Anthu ena amatumizilana mameseji, mapikica, kapena mavidiyo pa foni okhudza zakugonana. Malinga na mmene zinacitikila, anthu ocita zimenezi angafunike kuwapangila komiti ya ciweluzo. Nthawi zina, ngakhale acicepele amene amacita khalidwe limeneli, angaimbidwe mlandu na boma. Kuti mudziŵe zambili, pitani pa jw.org (ku Chichewa), na kuŵelenga nkhani yakuti, “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?” (Onani pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACINYAMATA.) Kapena onani nkhani yakuti, “Kukambirana ndi Mwana Wanu Nkhani Yotumizirana Zinthu Zolaula,” mu Galamukani! ya November 2013, mape. 4-5.