Mawu Amunsi
a Pulofesa Marvin Pate analemba kuti: “Anthu akhala akukhulupilila kuti mawu akuti ‘lelo’ pa lembali amakamba za tsiku la maola 24. Koma mfundo imeneyi imatsutsana na zimene mavesi ena a m’Baibo amakamba, cifukwa amaonetsa kuti Yesu atafa, coyamba ‘anatsikila ku manda, (Mat. 12:40; Mac. 2:31; Aroma 10:7) ndipo pambuyo pake anaukitsidwa na kupita kumwamba.”