Mawu Amunsi
a Ngati timaonetsa ena cifundo mu ulaliki, tingawonjezele cimwemwe cathu, komanso anthu angakhale ofunitsitsa kumvetsela uthenga wathu. N’cifukwa ciani zili conco? M’nkhani ino, tidzakambilana zimene tiphunzilapo pa citsanzo ca Yesu. Tidzakambilananso njila zinayi zimene tingaonetsele cifundo kwa anthu amene timapeza mu ulaliki.