Mawu Amunsi
a Satana na ziŵanda zake amasoceletsa anthu mwa kugwilitsila nchito mabodza osiyana-siyana onena za akufa. Mabodza amenewa apangitsa kuti pakhale miyambo yambili yosemphana na Malemba. Nkhani ino idzakuthandizani kudziŵa zimene mungacite kuti mukhalebe okhulupilika kwa Yehova ngati anthu ena akukakamizani kucitako miyambo yotelo.