Mawu Amunsi
a Tonse timafuna kuti abululu athu adziŵe Yehova. Koma iwo ali na ufulu wosankha kutumikila Yehova kapena ayi. M’nkhani ino, tikambilane zimene tingacite kuti cikhale cosavuta kwa abululu athu kumvetsela uthenga wathu.