Mawu Amunsi
b Zofukiza zimene zinali kufukizidwa pa cihema zinali kukhala zopatulika, ndipo Aisiraeli akale anali kuzigwilitsila nchito kokha pa kulambila Yehova. (Eks. 30:34-38) Koma palibe umboni uliwonse woonetsa kuti Akhristu a m’nthawi ya Atumwi anali kufukiza zofukiza pa kulambila kwawo.