Mawu Amunsi
h MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI:Mu February 2019, M’bale Gerrit Lösch wa m’Bungwe Lolamulila, anatulutsa Baibulo la Dziko Latsopano lokonzedwanso la Cijelemani. Masiku ano, ofalitsa ku Germany, monga alongo aŵiliwa, amakondwela kuseŵenzetsa Baibo yokonzedwanso mu ulaliki.