Mawu Amunsi
a Kungoyambila pa Pentekosite wa mu 33 C.E, Yehova wakhala akupatsa Akhristu ena ciyembekezo capadela cokalamulila na Mwana wake kumwamba. Koma kodi iwo amadziŵa bwanji kuti asankhidwa kukalamulila na Yesu kumwamba? Nanga n’ciani cimacitika munthu akadzozedwa? Nkhani ino ni yozikidwa pa nkhani ya mu Nsanja ya Mlonda ya January 2016, ndipo idzayankha mafunso ocititsa cidwi amenewa.