Mawu Amunsi
e MAWU OFOTOKOZELA CITHUNZI: Kaya tinaikidwa m’ndende cifukwa ca cikhulupililo cathu, kapena tili na mwayi wolalikila na kuphunzitsa coonadi mwaufulu, timayembekezela mwacidwi kudzakhala na moyo pano dziko lapansi, pamene Ufumu wa Mulungu udzayamba kulamulila.