Mawu Amunsi
b M’nkhani zakuti “Baibo Imasintha Anthu,” muli zitsanzo zambili zoonetsa mmene anthu amasinthila umoyo wawo. Nkhanizi zinali kupezeka mu Nsanja ya Mlonda, koma zinaleka kutuluka m’magazini mu 2017. Lomba zimafalitsidwa pa jw.org®. Onani ku Chichewa pa ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA.