Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pamene m’bale na mkazi wake alalikila ku nyumba na nyumba, aona (1) pa nyumba posamalidwa bwino komanso pokongoletsedwa na maluŵa; (2) pa nyumba pamene pali ana aang’ono; (3) pa nyumba posasamalidwa bwino kunja na mkati momwe; komanso (4) pa nyumba ya anthu opembedza. Kodi ni pa nyumba iti pamene muona kuti mungapeze munthu amene angakhale wophunzila wa Yesu mosavuta?