Mawu Amunsi
a Kwa zaka zambili, takhala tikukhulupilila kuti ulosi wa m’macaputa 1 na 2 a buku la Yoweli, umakamba za nchito yolalikila imene tikugwila masiku ano. Koma pali zifukwa zinayi zomveka bwino zimene zionetsa kuti tifunika kusintha kamvedwe kathu ka ulosi wa m’macaputa amenewa a buku la Yoweli. Kodi zifukwa zimenezo n’ziti?