Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mdyelekezi ananeneza Mulungu. Anauza Hava kuti Mulungu ni wabodza. Kwa zaka zambili, Satana wakhala akufalitsa mabodza, monga lakuti Mulungu ni wankhanza. Komanso kupitila m’ciphunzitso ca cisanduliko, Satana amaphunzitsa anthu kuti Mulungu sindiye analenga anthu.