Mawu Amunsi
a Masiku ano, tikukhala m’dziko lodzala ndi anthu odzikuza komanso odzikonda. Koma tiyenela kukhala osamala kuti tisatengele makhalidwe awo. M’nkhani ino, tikambilana mbali zitatu zokhudza umoyo wathu, ndipo pa mbali zimenezo, tiona mmene tingaonetsele kuti sitidziganizila kuposa mmene tiyenela kudziganizila.