Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Munthu wodzikuza amadziona kuti ni wofunika kwambili kuposa ena. N’cifukwa cake amakhalanso wodzikonda. Koma wodzicepetsa amakhala wosadzikonda. Kudzicepetsa kumatanthauza kusakhala wonyada komanso kusadziona kuti ndife ofunika kwambili kuposa ena.