Mawu Amunsi
b Kuti mudziŵe zimene mungacite pokambilana na ena mfundo zoyambilila za m’Baibo, onani nkhani zakuti “Kukambilana Ndi Munthu Wina Nkhani za m’Baibulo,” zopezeka mu Nsanja ya Mlonda kuyambila mu 2010 mpaka mu 2015. Muli nkhani monga zakuti “Kodi Yesu Ndi Mulungu?” “Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulila?” komanso yakuti “Kodi Mulungu Amalanga Anthu Kumoto?”