Mawu Amunsi
a Munthu wodzicepetsa amakhala wacifundo. Conco, m’pomveka kukamba kuti Yehova ni wodzicepetsa. M’nkhani ino, tikambilana zimene tingaphunzile kwa Yehova pa nkhani ya kudzicepetsa. Tikambilananso zina zimene tingaphunzile pa nkhani ya kudzicepetsa kwa Mfumu Sauli, mneneli Danieli, komanso Yesu..