Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mkulu akuphunzitsa m’bale wacinyamata nchito yosamalila magawo a mpingo. M’kupita kwa nthawi, mkuluyo akumulola m’bale wacinyamatayo kugwila yekha nchitoyo popanda kumuyang’anila pa ciliconse cimene akucita.