Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mlongo akufunsila malangizo kwa mkulu kuti adziŵe ngati n’koyenela kukapezeka pa cikwati cocitikila m’chechi. M’malo mofotokoza maganizo ake, mkuluyo akuonetsa mlongoyo mfundo za m’Baibo zimene angatsatile.