Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Munthu amene anamwalila zaka mahandiledi zapitazo, waukitsidwa mu Ulamulilo wa Khristu wa Zaka 1,000. M’bale amene anapulumuka pa Aramagedo akuphunzitsa munthu woukitsidwayo zimene afunika kucita kuti apindule na nsembe ya dipo la Khristu.