Mawu Amunsi
a Yesu anaitana asodzi odzicepetsa komanso akhama kuti akhale ophunzila ake. Masiku anonso, iye akupitiliza kuitana anthu amene ali na makhalidwe amenewa kuti akhale asodzi a anthu. M’nkhani ino, tikambilana zimene ophunzila Baibo amene amazengeleza kulabadila ciitano ca Yesu ayenela kucita.