Mawu Amunsi
a M’nkhani ino tikambilane njila zitatu zimene Yehova anaseŵenzetsa pothandiza mtumwi Paulo kulimbana na mavuto. Kuphunzila mmene Yehova anakhalila Mthandizi kumbuyoko, kudzalimbitsa cikhulupililo cathu cakuti Yehova adzatithandizanso masiku ano pamene tikulimbana na mavuto.