Mawu Amunsi
a Lemba la caka ca 2021 ligogomeza kufunika kodalila Yehova pamene tikulimbana na mavuto odetsa nkhawa palipano, komanso kutsogolo. M’nkhani ino, tikambilane njila za mmene tingaseŵenzetsele uphungu wa m’lemba lathu la caka.