Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mutu wa banja amene ali na zocita zambili, atengako mbali pa nchito yothandiza pakagwa tsoka, acilikiza nchito ya padziko lonse mwa zopeleka zake, komanso waitanila ena kuti akhale nawo pa kulambila kwa pabanja pamodzi na mkazi wake na ana ake.