Mawu Amunsi
a Kodi alongo ali na mbali yanji mumpingo? Kodi m’bale aliyense ni mutu wa mlongo aliyense? Kodi akulu na mitu ya mabanja ali na ulamulilo wolingana? M’nkhani ino, tikambilana mafunso amenewa mogwilizana na zitsanzo zopezeka m’Mawu a Mulungu.