Mawu Amunsi
a Ena a ife tilibe mwayi wotsogoza phunzilo la Baibo palipano. Ngakhale n’telo, aliyense wa ife angathe kuthandiza wina kupita patsogolo kuti akabatizike. M’nkhani ino, tione mmene aliyense wa ife angathandizile wophunzila Baibo kukwanilitsa colinga cimeneco.