Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tikambilane mmene cikondi pa Yehova, pa alambili anzathu, komanso ngakhale pa adani athu cimatithandizila kugonjetsa cidani ca dziko. Tionenso cifukwa cake Yesu anakamba kuti tingakhalebe acimwemwe ngakhale pamene tizondewa.