Mawu Amunsi
a Monga mmene ikambila Mateyu 17:5, Yehova amafuna kuti tizimvela Mwana wake. M’nkhani ino, tikambilana zina mwa zimene tingaphunzile pa zimene Yesu anakamba atatsala pang’ono kufa pa mtengo wozunzikilapo.