Mawu Amunsi
a M’nkhani yapita, tinakambilana zifukwa zinayi zimene anthu anakanila Yesu m’nthawi yakale, na zimene iwo amakanila otsatila ake masiku ano. M’nkhani ino, tikambilananso zifukwa zina zinayi. Tionanso cifukwa cake anthu oona mtima amene amakonda Yehova sapunthwa.