Mawu Amunsi
a Monga mmene mbiya ya ming’alu siikhala yolimba, mpingonso umakhala wagwede-gwede ngati muli mzimu wampikisano. Ngati mpingo si wogwilizana, sungakhale malo a mtendele olambililapo Mulungu. M’nkhani ino, tikambilane cifukwa cake tifunika kupewa kuyambitsa mzimu wampikisano, komanso zimene tingacite kuti tilimbikitse mtendele mu mpingo.