Mawu Amunsi
a Yehova satiyelekezela na ŵena. Komabe, tingayambe kudziyelekezela na ŵena na kuyamba kuona kuti siticita bwino. M’nkhani ino, tikambilana cifukwa cake si kwabwino kudziyelekezela na ŵena. Tionenso mmene tingathandizile a m’banja lathu na ŵena mu mpingo kudziona mmene Yehova amawaonela.