LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO

Mawu Amunsi

b MAWU OFOTOKOZELA CITHUNZI: Kungoyambila ali mwana, mlongo wakhala akupemphela kwa Yehova. Ali mwana, makolo ake anamuphunzitsa mopemphelela. Ali wacitsikana anayamba upainiya, ndipo nthawi zonse anali kupempha Yehova kuti adalitse utumiki wake. Pambuyo pa zaka, mwamuna wake atadwala, akucondelela Yehova kuti amupatse mphamvu zofunikila kuti apilile ciyeso cimeneco. Lelo lino, monga mkazi wamasiye, iye akupitiliza kupemphela, ali na cidalilo cakuti Atate wake wakumwamba, adzayankha mapemphelo ake monga mmene akhala akucitila mu umoyo wake wonse.

Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
Tulukani
Loŵani
  • Cinyanja
  • Gawilani
  • Makonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenela Kutsatila
  • Mfundo Yosunga Cisinsi
  • Kusunga Cinsinsi
  • JW.ORG
  • Loŵani
Gawilani