Mawu Amunsi
d Abale obatizika akulimbikitsidwa kugwila nchito molimbika mu mpingo kuti ayenelele kukhala atumiki othandiza kapena akulu. Kuti mudziŵe ziyenelezo zimene mufunika kukwanilitsa, onani mutu 5 na 6 m’buku lakuti, Gulu Lokhazikitsidwa Kucita Cifunilo ca Yehova.