Mawu Amunsi
a Yehova ndiye gwelo la zabwino zonse. Iye amapatsa zabwino anthu onse, kuphatikizapo oipa. Koma maka-maka amakonda kucitila zabwino alambili ake okhulupilika. M’nkhani ino, tione mmene Yehova amaonetsela ubwino wake kwa atumiki ake. Tionenso mmene awo amene amawonjezela utumiki wawo amapindulila na ubwino wa Yehova.