Mawu Amunsi
a Kaya ciyembekezo cathu n’cakumwamba kapena padziko lapansi la paladaiso, timayembekezela mwacidwi kupezaka pa Cikumbutso caka ciliconse. Nkhani ino, ifotokoza zifukwa za m’Malemba zimene timapezekela pa Cikumbutso, na mmene timapindulila tikatelo.