Mawu Amunsi
a Kuti tiyenelele ubatizo, tiyenela kuyesetsa kusintha umunthu wathu. Nkhani ino, itithandiza kudziŵa makhalidwe amene amapanga umunthu wakale, cifukwa cake tiyenela kuvula umunthu wakale umenewo, komanso mmene tingacitile zimenezo. Nkhani yotsatila, idzafotokoza mmene tingapitilizile kuvala umunthu watsopano, ngakhale pambuyo pa ubatizo.